Phungu wakunyumba yamalamulo wamdera la Zomba Malosa Grace Kwelepeta wafunira mafuno abwino ophunzira a standard 8 a sukulu zomwe zikupezeka m'dera lake omwe ayamba kulemba mayeso omaliza opitira ku sekondale omwe amayendetsedwa ndi Bungwe lomwe limawona zamayeso la Malawi National Examination Board (MANEB) Kwelepeta walimbikitsa ophunirawa kuti alembe mtima ulipansi ndipo ayike Mulungu patsogolo panthawi […]
The post Phungu wa Zomba Malosa afunira mafuno abwino ophunzira a Standard 8 appeared first on Malawi 24.