Ati mukamva za anthu osowa, kenako kuzindikira kuti aphedwa, muzingokhala chete basi ndi kumati Chakwera 2025 boma. Ati kufalitsa nkhani za kusowa kwa chitetezo mu dziko muno mutha kupezeka nazo ku jele. Atero ndi a nduna a za chitetezo a Zikhale Ng'oma. Polankhula pa msonkhano wa atolankhani umene anachititsa ku Lilongwe, a Ng'oma ati mu […]
The post Mukamakamba za kupanda chitetezo mu dziko muno tikumangani - watero Zikhale appeared first on Malawi 24.