Mtsikana wa wazaka 16 m’boma la Mzimba wadzipha podzimangilira mu mtengo pafupi ndi nyumba yakwawo kamba koti mayi ake anamukalipira chifukwa chomwa mowa mwauchidakwa tsiku la khilisimisi. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ku Jenda m’bomali a Macfaren Mseteka, nkhaniyi yachitika pa dera lotchedwa Mqocha m'boma la Mzimba ndipo iwo azindikira malemuwa ngati Kellness Kajani […]
The post Mtsikana wadzikhweza atakalipilidwa kamba komwa mowa pa khilisimisi appeared first on Malawi 24.