Nthambi yowona za anthu olowa ndi otuluka m'dziko muno ya DICS, yati ntchito yobwezeretsa sisitimu yake yomwe inasokonezedwa ndi akathyali ena ikubala zipatso ndipo akuti pali chiyembekezo chokwanilitsa ntchitoyi asanathe masiku 21 omwe anapeleka mtsogoleri wa dziko lino. Izi zikubwera pomwe kuyambira January chaka chino, nthambiyi siyikukwanitsa kugwira ntchito zake zina kuphatikiza kusindikiza ziphaso zoyendera […]
The post Immigration yati kubwezeretsa sisitimu kukutheka appeared first on Malawi 24.