Ati mukamayenda mumseu ndi kumuona mtsogoleri wa dziko lino muzikhala kuti mukuona tate wa akuba onse ndithu. Watelo mtsogoleri opuma a Peter Mutharika. Polankhula pa msonkhano wa atolankhani ku nyumba yawo ku Mangochi, a Mutharika ati a Chakwera asokoneza dziko la Malawi ndipo akupanga zinthu zimene ankanyoza nawo a Mutharika. 'A Chakwera kunasowa 6.2 biliyoni […]
The post Chakwera, ndiwe tate wa mbava - watelo Mutharika appeared first on Malawi 24.