Mtsogoleri wakale wa dziko lino Dr Joyce Banda wanyamuka lero kupita mdziko la Kenya komwe watumidwa ndi a Lazarus Chakwera kukawaimilira pa maliro a mtsogoleri wakale wa dzikolo a Mwai Kibaki. A Kibaki omwe anali ndizaka 90, anamwalira lachinayi sabata yatha pa 21 April ndipo thupi lawo likuyembekezeka kulowa mmanda loweluka lino pa 30 April. […]
The post Chakwera atuma Joyce Banda ku maliro appeared first on Malawi 24.