Mtsogoleri wa dziko lino la Malawi a Lazarus Chakwera wadzudzula mchitidwe wa anthu ena osagwira ntchito kaamba kodalira thandizo lochokera kwa anthu andale ponena kuti mchitidwewu ukukolezera khalidwe loba ndalama zaboma. A Chakwera amayankhula izi lolemba ku BICC mumzinda wa Lilongwe komwe amakhazikitsa gawo loyamba la zaka khumi la masomphenya a dziko lino pofika chaka […]
The post Chakwera ati andale amaba ndalama zaboma akamapemphedwa zinthu appeared first on Malawi 24.