Bwalo lamilandu ku Zomba layimitsa mulandu wa wapolisi wina Sergeant Twaliki Paweni yemwe akumuzenga mulandu chifukwa chomuganizira kuti adagwilira mtsikana wa zaka 14 mwezi wa August chaka chatha. Paweni akumuganizira kuti adapanga za upanduzi pa nthawi yomwe mtsikanayu adali m'manja mwa apolisi ndipo adamuwuza usiku kuti agone naye kuti amutulutse akhale mfulu. Mbali ya boma, […]
The post Bwalo liyimitsa mulandu wa wapolisi mpaka lachitatu sabata yamawa appeared first on Malawi 24.