Mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering International Prophet Shepherd Bushiri walengeza kuti ayambiranso kugawa chakudya kwa anthu opitilira 1 miliyoni omwe akhudzidwa ndi njala mdziko muno. Malinga ndi mneneri Bushiri, ndondomekoyi ipulumutsa Amalawi mamiliyoni ambiri omwe akhudzidwa ndi njala pazifukwa zosiyanasiyana monga Cyclone Freddy. Bushiri wapempha mabungwe akuluakulu aboma ndi anthu onse kuti awonetsetse […]
The post Bushiri watulukira! Agawa chimanga kwa anthu opitilira 1 million, chokwana K14 billion appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.