Boma lati ndalama zokwana K800 miliyoni ziperekedwa ku ntchito yomangira mabwalo amasewero a FCB Nyasa Bullets ndi Mighty Mukuru Wanderers. Nduna ya zamasewero Uchizi Mkandawire ndi yomwe yanena izi lero. Malingana ndi a Mkandawire, ntchitoyi inaima m'mbuyomu kamba ka ngongole zina zomwe makontilakitara a mabwalowa anali nazo komanso kukwera mitengo kwa zipangizo zina zogwilira ntchitoyi. […]
The post Boma lati mabwalo a Bullets ndi Wanderers amangidwa appeared first on Malawi24.