Ku mpingo wa Mibawa CCAP omwe uli pansi pa sinodi ya Blantyre kunabuka nkangano mpingowu utakana kuyimbila maliro a membala wake ponena kuti amamwa mowa. Malingana ndi lipoti ya MBC, abale a munthu omwalirayo komanso ena omwe amakhala mozungulira derali anayamba kugenda komanso kufuna kutentha tchalitchi cha Mibawa CCAP ponena kuti chakana mkhristu wawo. Akuluakulu […]
The post Apolisi athila utsi okhetsa misozi kutabuka zipolowe ku mpingo wa Mibawa CCAP appeared first on Malawi 24.