Katswiri pa nkhani za ndale, Thomas Chirwa, yemwenso ndi mphunzitsi pa sukulu ya ukachenjede ya (University of Dar Es Salaam) koma ndi M'malawi wati ndipovuta kuti andale azipani zotsutsa asiye kumayankhula za imfa ya yemwe adali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima pa misonkhano yawo. Chirwa wati ngati anthu akuyankhula kwambiri nkhani […]
The post Anthu adzilankhulabe za imfa ya Chilima - Chirwa appeared first on Malawi 24.