Mu buku la Mafumu mu Baibulo ati muli nkhani ya Eliya, amene anapemphela ataona ng'amba. Mtsogoleri opuma wa dziko lino a Peter Mutharika ati a Malawi akuyenela kuchita monga anachitila Eliya: kugwada mozichepsa pa maso pa Chauta. A Mutharika ati kusowa kwa mvula mu dziko lino tsopano kwafika poopsa ndipo a Malawi onse ayenela apinde […]
The post Amalawi, pemphelani kosalekeza - watelo Mutharika appeared first on Malawi 24.