Alimi okhala ku Mpemba mu mzinda wa Blantyre, ali mkati mobzala mbeu nzawo kutsatira Mvula ya mphamvu yomwe inagwa m'derali mu usiku wa pa 9 November, 2023. Bambo silika ochokera m’mudzi mwa Mkoma m'dera la mfumu yaikulu Mtonda mu mzinda wa Blantyre ndi m'modzi mwa alimi amene ali mkati mobzala mbeu zawo ndipo iwo ati […]
The post Alimi ayamba kubzala ku Mpemba appeared first on Malawi 24.