Atsikana ndi amayi akugonana ndi asodzi pa doko la Bulawayo ku Nsanje n'cholinga choti aziwapatsa milamba ndi makakana. Mkulu woona za ntchito yolimbana ndi edzi a MacKnowledge Tembo komanso woona za ntchito yogawa makondomu m'bomalo a John Maganizo ndiwo atulutsa nkhaniyi patsiku lokumbukira kufunika kwa makondomu pa msika wa Sorgin m'bomalo. 'Atsikana ndi amayi […]
The post Zoopsa! Azimayi, atsikana akugonana ndi asodzi kuti aziwapatsa milamba, makakana appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.