Mmodzi wa anthu amene akufuna kupikisana nawo pa udindo wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha MCP a Vitumbiko Mumba walonjeza kuthandiza Blantyre CCAP Synod m'magawo osiyanasiyana. A Mumba ayankhula izi pa mpingo wa Mount Carmel CCAP mu mzinda wa Blantyre pamene adali nawo pa mwambo wolandira a Anderson Juma kukhala m'busa wa mpingowu. Mwazina, […]
The post Vitumbiko Mumba wapita basi! BT CCAP yati ndiyokondwa ndi iyeyu chifukwa utsogoleri ulimo mwanyamatayi appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.