Chipani cha UTM chati mgwirizano wawo ndi MCP pa yemwe akudzaimira mgwirizano wa Tonse mu chisankho chikudzachi sudasinthe ndipo ‘udakali chimodzimodzi’. Mlembi wamkulu wa UTM, Patricia Kaliati, watiuza kuti adagawana zaka zisanu kwa otsogolera aliyense ndipo kuti mfundoyi sidachitike ndi atsogoleri a zipani ziwiri zokhazi ayi koma kuti otsatira ena adavomereza. Malingana ndi Kaliati, mgwirizanowu […]
The post UTM ikuti mgwirizano wawo ndi MCP ukadali chimodzimodzi appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.