Apolisi munzinda wa Lilongwe amanga mmodzi mwa anthu odziwika bwino pamasamba amchezo Hannah Jabes, yemwe amadziwika bwino ndi dzina la Tamia Ja, kamba kankhani yogwirizana ndi kuba. Malingana ndi a polisi, masiku angapo apitawo analandira dandaulo kuchokera kwa mkulu wina wochita malonda yemwe anati Tamia Ja anazambayitsa ndalama zokwana 8 million kwacha zitaikidwa molakwika mu […]
The post Tamia Ja amangidwa poganiziridwa kuti anazembeyesa K8 miliyoni ya mwini appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.