Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera dzulo anathawa funso lokhudza kusakazidwa kwa ndalama ku National Oil Company of Malawi (NOCMA) kudzera mu chitetezo chomwe chikuperekedwa kwa a Hellen Buluma. A Chakwera, omwe NOCMA ili pansi pa unduna wawo wa Mphamvu za Magetsi, ananena izi pa msokhano wa atolankhani dzulo. Ma lipoti anamveka masabata apitawa […]
The post Sindikudziwa – Chakwera athawa funso la NOCMA appeared first on Malawi 24.