Pulezidenti Lazarus Chakwera watsimikizira a Malawi kuti boma lake lipitiriza kupereka zitukuko mosatengera chigawo kapena mtundu wa anthu. Polankhula m’boma la Rumphi pomwe amatsegulira sukulu zitatu zosula aphunzitsi m’maboma a Chikwawa, Mchinji ndi Rumphi, Chakwera anati ndi cholinga cha boma lake kuti dera lililonse lilandire chitukuko mofanana. Mtsogoleriyu anati ichi ndi chifukwa chake boma lake […]
The post Nditukula Malawi mosatengera chigawo, mtundu wa anthu – Chakwera appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.