Chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) chabwezeretsa akuluakulu anayi omwe chinawachotsa mu mchipanichi komaso pa maudindo awo kaamba kosasunga mwambo. A Kondwani Nankhumwa omwe ndi mtsogoleri wachipanichi mchigawo chakummwera, mlembi wa mkulu a Grezelda Jeffrey, msungichuma wamkulu a Jappie Mhango komaso a Yusuf Nthenda, anachotsedwa mchipanichi mwezi wa October chaka chatha. Potsatira izi, anayiwa […]
The post Nankhumwa, Grezelda ndi ena awiri awabwezeretsa mu DPP appeared first on Malawi 24.