Mabungwe a National Aids Commission (NAC) ndi Pharmacy and Medicines Regulatory Authority (PMRA) ati ndiokhumudwa ndi kufala kwa mchitidiwe ofalitsa mauthenga abodza okhudza matenda a edzi kudzera mmasamba a mchezo monga TikTok, Facebook komanso WhatsApp. Wamkulu wa bungwe ka NAC, Mayi Beatrice Matanje wawuza atolankhani mu mzinda wa Lilongwe kuti kafukufuku wa posachedwa yemwe mabungwe […]
The post Mabungwe a NAC, PMRA akhumudwa ndi kufala kwa mauthenga a bodza a mankhwala a HIV appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.