Malipoti omwe akungotipeza kumene akusonyeza kuti Khonsolo la Mzinda wa Lilongwe layambapo ntchito yosamutsa mtaya wa zinyalala kuchokera ku dela 38 mumzindawu. Mfumu yamzinda wa Lilongwe Khansala Richard Banda ndi imene yanena izi lero pa nsonkhani wa atolankhani mumzinda wa Lilongwe. A Banda anati Khonsolo yalemba kale ntchito anthu yowunika zonse zokhudza ntchito yosamutsa mtayayi. […]
The post Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe iyamba ntchito yosamutsa mtaya appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.