Wolemba: Gracious Zinazi Anthu mazanamazana anadzadza mu misewu ya mu mzinda wa Dakar ku Senegal dzulo kukalandira osewera a timu ya dziko lawo omwe atenga chikho cha AFCON. Tsiku la 6 February 2022 ndilosaiwalika kwa mzika za dziko la Senegal chifukwa team ya dzikoli inagonjetsa Egypt mu mpikisano wa African Cup of Nations ku Cameroon […]
The post Chikho cha AFCON chalandiridwa mopatsa chidwi ku Senegal appeared first on Malawi 24.