A George Chaponda, omwe ndi mtsogoleri otsutsa boma ku nyumba ya malamulo, wauza President Lazarus Chakwera kuti atulutse nsanga zotsatira za kafukufuku wa ngozi ya ndege yomwe idapha a Saulos Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu pa 10 June chaka chino. A Chaponda ati a Chakwera adauza mtolankhani wa DW kuti akatswiri aku Germany […]
The post Chaponda akuti a Chakwera atulutse lipoti la Ngozi ya ndege ku Chikangawa appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.