Tate wa pfuko la Malawi , Dr Lazarus McCarthy Chakwera lero wapereka katundu osiyana siyana kwa anthu omwe akubvutika ndi madzi osefuka mboma la Karonga. Chakwera wapereka ufa , ziwiya zophikira , ndiwo ndi katundu winanso kwa ndi cholunga choti anthu kumeneko athandizike mdelaro. Poyankhula atayendera misasa ya Kambwe ku Karonga, komweko , mtsogoleri wa […]
The post Chakwera athandiza anthu omwe akhudzidwa ndi ngozi yodza kamba kosefukira kwa madzi appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.