Bambo wa zaka 27 yemwe dzina lake ndi Makaiko Moyo Chimkute amumanga ku Mchinji chifukwa chogwirilira mwana wa zaka 14. Malingana ndi wofalitsa nkhani za apolisi ku Mchinji a Limbani Mpinganjira, anthu awiri-wa anayamba kucheza pa tsamba la facebook ndipo dzulo bamboyo anayitana mnyamatayo kunyumba kwake pomulonjeza kuti amugulira zakumwa zoziziritsa ku khosi. Pa 5 […]
The post Bambo wa zaka 27 amumanga chifukwa chogwirilira mnyamata appeared first on Malawi24.