Unduna owona za ubale wa dziko lino ndi mayiko ena walengeza kuti lero pa 10 June 2024, Chakwera anyamuka pa ulendo opita m'dziko la Bahamas komwe akukakhala nawo pa nsonkhano wa pachaka wa zamalonda omwe wakozedwa ndi AFREXIMBANK komanso Afri-Caribbean Trade and Investment Forum. Malingana ndi undunawu, nsonkhanowu ukachitikira munzinda wa Nassau kuyambira Lachitatu pa […]
The post Wa mlengalenga kachikena, Chakwera alunjika ku Bahamas ndi ku Switzerland appeared first on Malawi 24.