Nthambi yoona za nyengo m’dziko muno ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yati mu mwezi wa October, madera ambiri akuyembekezereka kulandira mvula yamlingo okhazikika kapena kuposera apo. DCCMS yati nyengo ya dzinja ku Malawi kuno imayamba mu October kufikira m’mwezi wa April ndipo nyengoyi imakhazikika m’mwezi wa November kuyambira kumwera kwadziko lino […]
The post Tiyembekezere mvula mwezi wa October – DCCMS appeared first on Malawi 24.