Yemwe anali katakwe womwetsa zigoli mu timu ya mpira ya dziko lino Kinnah Phiri wauza Malawi24 kuti timu ya Flames ingakwanitse kupita ku AFCON pamaso pa Senegal komanso Burkina Faso, omwe ali mu Gulu L. Kinnah Phiri akukhulupirira kuti timu ya Flames siili m’gulu lowopsa pangofunika kukonzekera bwino ndi kusankha wosewera abwino zikatero Flames akhoza […]
The post Timu ya Malawi silili m’gulu la imfa - Kinnah Phiri appeared first on Malawi 24.