Nduna yowona za malimidwe a Sam Kawale ati boma likhala likupitiliza kutumiza chimanga chimene likusunga mu nkhokwe zake ku misika ya ADMARC m'dziko muno ngakhale anthu pakali pano ayamba kukolola chimanga m'minda yawo madela ena. A Kawale amayankhula izi m'nyumba ya malamulo pamene Phungu wa nyumba ya malamulo ku m'mawa kwa boma la Chiradzulu anafunsa […]
The post Tikutumiza chimanga chochepa dala pofuna kuteteza ku mbava – Sam Kawale appeared first on Malawi 24.