Banki yaikulu m'dziko muno ya Reserve (RBM) yatsutsa mphekesera zomwe zikumveka kuti ikufuna ichepetseso mphamvu za ndalama ya dziko lino. Nkhaniyi ikudza pomwe pamasamba a mchezo pakhala pakuzungulira mphekesera yoti RBM ikufuna kutsitsanso mphamvu ya ndalama ya Kwacha kumapeto a mwezi uno. Mphekeserazi zimasonyeza kuti bankiyi ikufuna kugwetsa mphamvu ya ndalama ya dziko lino ndi […]
The post Sitikugwetsanso Kwacha – yatsutsa RBM appeared first on Malawi 24.