Woyimba Noel Chikoleka yemwe adayimba nyimbo ya “Makofi” ndipo amadziwika kwambiri ndi dzina loti Phyzix, watsutsa mphekesera zoti iye adamenya woyimba nzake Pop Young chifukwa chokakamiza nkazi yemwe adapita naye kokayimba kuti amulore chibwezi. Potsatira mphekeserazi zomwe zakhala zikuveka m’masamba anchezo, Phyzix watulutsa chikalata chofotokoza momwe zinakhalira ku malo ochitira zisangalaro a Blues Elephant munzinda […]
The post Sindidamenye Pop Young – wakanitsitsa Phyzix appeared first on Malawi 24.