Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Mighty Mukuru wanderers Nsazurwimo Ramadhani wazisiya, watula pansi undindo wake patangotha myezi yosaposa inayi chibweleleni ku timuyi. Mphunzitsiyu yemwe watsogolera masewelo asanu ndi atatu okha (8) watula pansi udindo wake ku timuyi itagonja kawiri motsagana. Ramadhani watsimikira Nyumba ina yolemba nkhani kuti watula pansi udindo ndipo anati ngati zotsatila zolongosoka […]
The post Ramadhani wazidomoka appeared first on Malawi 24.