M'modzi mwaoyimba achizimayi odziwika bwino mdziko muno Tunosiwe Mwakalinga, yemweso anakhalapo chiphadzuwa cha mzinda wa Blantyre, wakwiyitsa azibambo pomwe wawanena kuti ambiri mphete zawo anaveka azimayi ogulitsa matupi. Mwakalinga yemwe amadziwika bwino kwambiri kuti Tuno lomwe ndi chidule cha dzina lake, anashosha kudambwe pomwe musabatayi analemba patsamba lake lamchezo la thwita kuti “Koma ma ring […]
The post Oyimba Tuno wati abambo akumaveka mphete mah*le appeared first on Malawi24.