Mpingo wa Anglican wauza Boma la Malawi kudzera ku unduna wa Zokopa alendo kuti zilumba za Likoma, Chizumulu komanso Mbamba sizili pamsika, ndipo zilumba zimenezi ndi za anthu omwe akukhalapo. Malinga ndi chikalata chomwe watulutsa Mpingowu chomwe chasayinidwa ndi RV. Fanuel Magangani, chitukuko chilichonse chomwe chifuna kupangika pa zilumba zi chizikhudza anthu okhala pompo kuti […]
The post Osatigulitsira Chilumba chathu - Mpingo wa Anglican wauza Boma appeared first on Malawi 24.