Timu ya Chombe Market Rangers yomwe ikusewera nawo mu mpikisano wa Castel Challenge ili pa chiopsezo choletsedwa kutenga nawo mbali mu mpikisanowu kapena kupatsidwa chindapusa cha ndalama zokwana K500,000 kamba koti osewera a timuyi adamenya komanso kuvulaza oimbira a MacNails Gausi, kutsatira kugonja 2-1 ndi timu ya Chibuku FC masanawa pa bwalo la Maganga. Izi […]
The post Oimbira mpira wavulazidwa ku Nkhata-Bay appeared first on Malawi 24.