Awa za ligi sizikuwakhudza. Za mpira ndi kutheka si mbali yawo. Chifukwa atagogodedwa sabata latha, leronso akhomedwa. Manoma ayenda wabule ku Mzuzu. Azibwelera chotsimphina. Mmalo motamangitsa matimu, iwo ndi amene akutamanga. Pa masewera amene akondoweza mzinda wa Mzuzu, timu ya Mzuzu City Hammers lero yaphunzitsa phunziro anyamata a Mighty Wanderers. Mavuto a nyerere anayamba chigawo […]
The post Neba mutu sukugwila: Mzuzu City Hammers 2, Wandalazi 0 appeared first on Malawi 24.