Mawu akulu akoma akagonera! Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Michael Usi, wasambira m’manja akuluakulu a chipani cha United Transformation Movement (UTM) pachipwilikiti chomwe chabuka m'chipanichi ponena kuti iye adawachenjeza kale konveshoni isanachitike. Usi wayankhula izi Lamulungu pomwe anakumana ndi anthu otsatira chipani cha UTM omwe anachokera ku Ndirande. Anthuwa anakhamukira ku nyumba ya Usi […]
The post Ndidakuuzani lero ndi izi, wayankhula Usi pakusavana ku UTM appeared first on Malawi 24.