Kampani yofulura bibida ya Castel yasutsa mphekesera zomwe zikumveka ndi anthu ena okonda chokumwa cha ukali kuti mowa wa gin wang'ono okhala mubotolo la 330ml ndiwamphamvu kuposa okhala mu botolo lalikulu la 750ml. Hammerson Kanyelere wa ku Lilongwe yemwe amakonda mowa waukaliwu wati gin wang'ono ndiwamphamvu kuposa wamkulu. 'Olo m'mene amawawira baby gin amaposanso gin […]
The post Mwanadala si wamphamvu kuposa mkulu wake - yatero Castel appeared first on Malawi 24.