Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ati chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chikukonza zoti chidzabele chisankho chosakha mtsogoleri wa dziko cha chaka cha mawa. A Mutharika amayankhula izi Lamulungu pa Njamba munzinda wa Blantyre pomwe chipani chawo cha Democratic Progressive Party (DPP) chinachititsa nsonkhano wa ndale. Poyankhula ku khwimbi la anthu lomwe […]
The post Mutharika wati MCP ikukoza zodzabera chisankho appeared first on Malawi 24.