M’modzi mwa anthu otchuka pa fesibuku, Pemphero Mphande wauza anthu onse omwe akunena kuti mzilazembe pa maimbidwe a Giddes Chalamanda akula asamakaimbe ku ma “show”, kuti ayambe kupeleka ndalama zothandizira umoyo wa tsiku ndi tsiku wa chiyambakaleyu. Chatsitsa dzaye kuti njobvu ithyoke nyanga nchakuti, lero lachisanu kuyambira 6 koloko madzulo, a Chalamanda akuyenera kukaimba kuphwando […]
The post Mukati a Giddes asamaimbe ku “show”, muziwadyetsa? - wang'alura Pemphero Mphande appeared first on Malawi 24.