Pamene anthu akudandaula kale ndi kukwera kwa mitengo yazinthu zambiri, boma kudzera kuunduna wa zachilengedwe laloleza mabungwe ogulitsa madzi mdziko muno kukweza mitengo. Izi ndimalingana ndi chikalata chomwe undunawu watulutsa posachedwapa chomwe wasainira ndi mlembi wamkulu kuundunawu a Yanira Mtupanyama. Mumchikalatachi, a Mtupanyama anati undunawu waloleza makampani ogulitsa madziwa ati kaamba koti mabungwe ogulitsa madziwa […]
The post Mitengo ya madzi yakwera appeared first on Malawi 24.