Mzimayi wina wa zaka 40 zakubadwa yemwe ndi mzika ya dziko la Zimbabwe watutumutsa anthu dzikolo atalengeza kuti ali ndi pakati ndipo bambo ake ndi mwana wake omubala wa zaka 23 zakubadwa. Betty Mbereko wa zaka 40 zakubadwa amakhala ndi mwana wake wa mwamuna, Farai Mbekero kamba koti bambo ake a Farai anamwalira zaka 12 […]
The post Mayi akwatirana ndi mwana wake omubereka appeared first on Malawi 24.