Akuluakulu a ofesi ya zaumoyo ku khonsolo ya m'boma la Dedza atsimikiza kuti madera a m'bomali mwabuka matenda a zilonda zapakhungu omwe ndi kuphatikizapo mphere zomwe ati zagwira anthu ochulukirapo. Malingana ndi ofalitsa nkhani ku ofesi ya zaumoyo m'bomali a Mwayi Liabunya, nkhaniyi ikutsatira zotsara za kuyezedwa kwa anthu ena omwe akudwala matenda apakhunguwa. A […]
The post Matenda a mphere avuta ku Dedza appeared first on Malawi 24.