Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati akubanja komanso abale a wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima apempha kuti pa mwambo wa maliro pasakhale ndale zilizonse potengera kuti eni akenso sakanakondwa kuti zitero. Poyankhura pa msonkhano wa atolankhani lero, a Kunkuyu ati akudziwa kuti anthu ambiri akonza zinthu zosokoneza pa mwambo wa […]
The post Malirowa musalowetse ndale- Kunkuyu appeared first on Malawi 24.