Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) lati likukhulupilira kuti a Malawi ali ndi ufulu wosankha kubayitsa kapena kusabayitsa katemera ndipo kubayitsa katemerayu kusakhale kokakamiza. Nkhawa ya bungwe la CDEDI ikubwera pomwe boma la Tonse motsogozedwa ndi mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera anena kuti ayamba kupereka katemera okakamiza kuyambira mu […]
The post Mabungwe akana mchitidwe obaya katemera mokakamiza appeared first on Malawi 24.