Kwacha aithyola kholingo, aikang’antha, aichotsa chimbenene, aikong’ontha, aichosa mphamvu. Banki yaikulu ya Reserve yanena lero kuti yachepetsa mphamvu ndalama ya Kwacha ndi ma pelesenti 25. Izi zikutanthauza kuti wani dollar ya ku America yomwe lero ikumafanana mphamvu ndi K825 ya Malawi, kuyambira mawa pa 27 May izifanana mphamvu ndi K1,031 ya ku Malawi. Kutsikaku kukutanthauzanso […]
The post Kwacha yada appeared first on Malawi 24.