Achitetezo akunyumba ya boma amenya khansala wachipani cha United Democratic Front (UDF) m'dela la Ruo m'boma la Nsanje, Mariko Mulotali. Izi zinachitika kum'mawaku pomwe khansalayu anamvedwa akunyoza utsogoleri wachipani cha Malawi Congress (MCP) nthawi yomwe mtsogoleri wadziko lino Lazarus Chakwera amakhazikitsa ntchito yomanga sukulu zatsopano za Makhanga Primary ndi Makhanga CDSS m'bomalo. Khansala Mulotali watsimikiza […]
The post Khasala amenyedwa ndi achitetezo a boma ku Nsanje appeared first on Malawi 24.