Kamuzu Barracks yapambana pamasewero omwe analiko lero mu TNM Super League pomwe imasewera ndi anyamata a Mighty Tigers ndi zigoli zitatu kwa ziwiri. Pa masewero omwe anachitikila pa Kamuzu Stadium, Kamuzu Barracks inapeza chigoli choyamba pa mphindi khumi komanso chigoli chachiwiri pamphindi makumi awili ndi anayi ndipo zonse anagoletsa ndi Zeliati Nkhoma. Kamuzu Barracks sinasiyire […]
The post Kamuzu Barracks yaswa timu ya Mighty Tigers appeared first on Malawi 24.